![]() |
Soldier of Christ Disciple Training Ministries |
|
BUKHU LAMULUNGU KWA ANTHU AMULUNGU |
|
| Akhristu amadziwika ndi dzina loti ‘Anthu a Bukhu’.Bukhuli ndi Baibulo chikhulupiliro chimalunjika m’baibulo komanso chakhazikikamo. Kodi mabukhu 66 ndiofunikira?Kodi chilamulo chake chimachokera kuti?Poyamba tione m’mene lasanjidwira. Baibulo lili m’magulu awiri chipangano chakale ndi chipangano chatsopano. Chakale muli mabuku 39 chatsopano muli mabuku 27. Chipangano chakale chili motere: Chilamulo- otchedwans mabuku a mose Mabuku asnu oyamba,Genesis,eksodo,numerindi Deuteronomy. Mabuku Ambiri: Amanene za za mbiri ya mulungu ndi anthu ake kuyambira nthawi yolowa m’dziko lalonjezano,kudutsa nthawi ya moweruza, mafumu a Isalieli ndi yuda, mpaka muukapolo kumalizira ndi Nehemia akumanganso Yelusasalemu mu 400BC.Mabukhu ake ndi Yoswa, Oweruza, Rute1&2, Samuel 1&2, Mafumu1&2, Mbiri, Ezara, Nehemia ndi Estere, ngakhale Estere amatsogozana ndi mabukhu anthano-Chipangano chakale-Yobu –Masalimo, Miyambo Mulaliki ndi nyimbo ya Solomo.Ngakhale zili ndakatulo sikuti simalemba oyera.Zasankhidwa potengera kalembedwe kake m’mene anasanjira mulibe mau ofanana koma kufanana kwa malingaliro ndi maganizo. Aneneri akuluakulu-siakulu chifukwa ndi ofunikira kwambiri kuposa a’gono koma malingana ndi kukula kwa mabuawo.Aneneri akul ;u alindimachaputala ochuluka kuposa an,gono an,gono- makuwa ndi Hosea, Yoweli, Amosi , Obadia, Yona, Mika, Nhumu, Habakuku, Zefania, Hagai, Zakaria ndi Malaki. Monga Chipangano chakale, chatsopanonso sichinasanjidwe mwandondomeko koma malingana ndi zomwe analemba. Uthenga wabwino, mateyu, Marko, Luke ndi Yohane ndi ma buku oyambirira.Atatu oyamba mateyu Marko ndi Luke ndi ofanana muuthenga wawo.Yohane analembedwa mosiyana ndi atatuwa komanso amaonetsera kufunika kwa uthenga wabwinowu. Mbiri ya ya mpingo- machitidwe Atumwi limalongosola za dongolo ,ndikukula kwa kwa mpingo komanso kukwera kwa Yesu. Makalata a Paulo- Paulo analemba theka lachipangano kuchokera mu zolemba zake zapangidwa aziphunzitsa zambiri komanso za gawidwa kukhala makalata opita kumpingo komanso kwa azitsogoleri polingana ndi maina .Aroma,1&2,Akorinto,Agalantiya, Aefeso, Afilipi, Akolose 1&2, Atesalonika1&2 Timoteo, Tito, Filimoni ndi Aheberi,Aheberi ali kumapeto ena amati Paulo sanalemba Aheberi koma zodziwika n’zoti analemba. Makalata ena-Awa analembedwa analembedwa ndi atumwi ndi olemba ena monga : Yakobo1&2 Petulo 1-2-3 Yohane ndi Yuda. Auneneri- Bukhu la Chivumulutso komanso lotsiliza.Dzina la Chivumbulkutso likutanthauza ‘kubvundukula’ Limavumbulutsa za yesu khristu komanso za Mtsogolo. Mabuku 66 ndi okhao omwe amatchuila za mulungu, tidzakamba kwambiri pa maphunziro odzilimbikitsa chimene takhulupirirea.Tsono tadziwa chomwe malembo ali tiyeni tione zomwe amakamba za iwo eni. Ine mulungu ndinauzira mpweya Paulo anati ‘malemba onse ndiouzilidwa ndimulungu’ zimene zikutanthauza kuti mulungu anatulutsa mpweya wa mulungu ndi umene umalimbikitsa olemba malemba. Ndichifukwa chake mulungu timati malemba onse mulungu anauzira mpweya.Paulo anakambanso zifukwa zina zomwe tiyenera kukhala ndi malemba.A nati ndiopindulitsa mu zinthu zambiri Chiphunzitso- Chiphunzitso chonse chimapezka m’mbaibulo. Pamene zikhulupiliro za bodza sizimayambira malemba oyera. Tiyenera kudarila malemba oyera komanso ndi malemba okhala kuti tipeze chiphunzitso.Chiphunzitso sichimangoyenera kunenedwa koma koma chiyeneleka kuphunzitsidwa tiyenera kuphunzitsa ena za mau amulungu. Kutsimikiza –kutathauza umbuni weniweni-kudzudzula winawake pogwilitsa ntchito malemba pofuna kuonetsera uchimom wawo.1Tim 5:20 2 Tim 4:2 Kulungamitsa – Kulungamitsa iwo amene achimwa –2 Tim 2:25, 4:2 Malangizo Achilungamo- Mau akuti kuphunzitsa mwana ndichizindikilo chimera kuphunzitsa obadwa kumene mwa tsopano chilungamo. Ndicholinga cha cha munthu wa ambvuye kukhala wamngwilo ndi ozikika kuka chita ntchito yabwino ya ambuye amene anatilenga (Aefeso 2:10)kuti mwa ichi ngati ambuye atiyitana pantchito yake tizikhala othekera komanso pa 2 Tim 3:15 Paulo akukumbutsa Timoteo kuti malemba ndi opindulitsa opatsa nzeru ya chipulumutso. MAU AMULUNGU Timathandauza chaini tikati baibulo ndi mau a Mulungu. Poyamba tione pamene Mulungu mwini wake akutchulidwa tikaona m’malemba tiona kuti mau akuti: “Atero ambuye” – Alembedwa kokwana ka 854 Mau Ambuye – Alipo 258 Ambuye anane –Alipo 144 Liu la Ambuye -alipo 49 Atate Analamuia –Alipo 14 Mulungu anati -Alipo 13 Ati Ambuye Alipo 12 Ambuye ayitana alipo 9 Mulungu ati –alipo 4 Ambuye alamula –Alipo4 Tsopano tikuona mau okwana 1,361 pa momwe mulungu amayankhula yekha ndipo tika gawa muzonse kuchokera pa 1,352 zomwe mulungu anayakhu tikuea kuti mulungu akuyamnkhula ka 20 mubukhu lilironse malemba sanagokha zimene mulungu anauzira koma mmalo okwana 1,000 akuti lamula ndi kutiuza oko ndiye kudabwitsa kwa bvku loyera ZOTSATIRA ZA MALEMBA PA ANTHU Baibulo ndi m’magawo ambiri anatsilizidwa komanso mulizolingalira anthu – Tiyeni tione mmene anthu osiyanasina analivomelezera po fufusa mmalembawa (mbiri) Tiyeni tiyambe ndi mfumu Yosiya pa 2 Mafumu 22 anali mfumu yabwino ndipo anayamba kulamulira ndi zaka 8. alikamwana anayamba kukonza kachisi wa Ambuye ntchitoyi ikupitilira anpeza buku lachilamuo limeneli anali mabuku asanu a chilamulo. Ansembe anayamba kumaiwrengera mfumu. Tione chimene chinachitika pamene mfumu inamca mau a chilamulo inang’amba zovala zake. Kenako inalamula Hilikiya wasembe nci ena asanu(antchito) kuti akafufusire iye ndi onse a mu yuda zokhudzana ndi buku limeneli chifukwa mkwiyo wa yehava utayakira ife ndi waukulu popeza atate wathu sanavere mau a m’buku. Mfumu inazinsikira kuti inali m’mabvuto inamva chilamulo, inamva chipangano chomwe chinalipo komanso zomwe anthu amayenera kuchita sizimachitika, inadziwa kuti ali muuchimo waukulu. Inadziwanso chiweluzo chake, inachita mantha choncho inatumiza antchito kukafufuza zomwe amayenera kumchitira ambuye. Umundimmene tiyenera kuchitira. Taonani chonadi cha Masalimo 19:7 malamulo a Yehova ali amngwiro akubwezera moyo “moyo wa Yosiya unasithika mu mtima mwake pamene anamva chilamulo chikwe werengedwa. Komanso Nehemia anawerenganso Buku la chilamulo ku wanthu a Isaleyi. Komanso anavomereza. Khamulonse linalira chifukwa chilamulo chinaonetsa uchimo wa kwa Mulungu Oyera. Bukuli ndilodzaza ndi mau a Mulungu kudzudzula ndi kusintha miyoyo a anthu. Zoonadi mau a Yehova ndi amoyo ndi ochita chita mongalupanga lakuthwa konsekonse palibenso buku la mphamvu ngati ili padzikolonse. Palibe buku lomwe lingaswe mtima wamunthu ndi kuudzadza ndi chiyembekezo nthawi yomweyo ngakha bukhu lachipembezo palibe lomwe lingasinthe moyo wa munthu ndi ku onetsera machimo ake. Kutsogoku tiona chifukwa chimene Yehova anatipatsira mau ake kuti tikakhulupire iye ndi kukhala ndi chikhulupiliro mwa iye. |
|